Oweruza 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pitani, kapempheni thandizo kwa milungu+ imene mwasankhayo.+ Milungu imeneyo ndi imene ikupulumutseni pa nthawi ya nsautso yanu.” Yesaya 46:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo amamunyamula pamapewa awo.+ Amamutenga n’kukamuika pamalo ake ndi kumuimika bwinobwino. Mulunguyo sayenda kuchoka pamalo akewo.+ Ngakhale munthu atamufuulira, iye sayankha. Sapulumutsa munthu kumavuto ake.+
14 Pitani, kapempheni thandizo kwa milungu+ imene mwasankhayo.+ Milungu imeneyo ndi imene ikupulumutseni pa nthawi ya nsautso yanu.”
7 Iwo amamunyamula pamapewa awo.+ Amamutenga n’kukamuika pamalo ake ndi kumuimika bwinobwino. Mulunguyo sayenda kuchoka pamalo akewo.+ Ngakhale munthu atamufuulira, iye sayankha. Sapulumutsa munthu kumavuto ake.+