Yesaya 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno kunyumba ya Davide kunapita uthenga wakuti: “Dziko la Siriya layamba kudalira dziko la Efuraimu.”+ Choncho mtima wa Ahazi ndi wa anthu ake unayamba kunjenjemera, ngati mmene mitengo ya m’nkhalango imagwederera ndi mphepo.+ Luka 1:69 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 69 Iye watikwezera ife nyanga*+ yachipulumutso m’nyumba ya mtumiki wake Davide,
2 Ndiyeno kunyumba ya Davide kunapita uthenga wakuti: “Dziko la Siriya layamba kudalira dziko la Efuraimu.”+ Choncho mtima wa Ahazi ndi wa anthu ake unayamba kunjenjemera, ngati mmene mitengo ya m’nkhalango imagwederera ndi mphepo.+