Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 25:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndiyeno munthu winawake wa Mulungu woona+ anapita kwa Amaziya n’kumuuza kuti: “Inu mfumu, musalole kuti gulu lankhondo la Isiraeli lipite nanu limodzi, chifukwa Yehova sali ndi Aisiraeli,+ kutanthauza ana onse a Efuraimu.

  • Yesaya 11:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Nsanje ya Efuraimu idzatha,+ ndipo ngakhale anthu odana ndi Yuda adzaphedwa. Efuraimu sadzachitira nsanje Yuda ndiponso Yuda sadzadana ndi Efuraimu.+

  • Ezekieli 37:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “Koma iwe mwana wa munthu, tenga ndodo+ ndi kulembapo kuti, ‘Ndodo ya Yuda ndi anzake, ana a Isiraeli.’+ Utengenso ndodo ina ndi kulembapo kuti, ‘Ndodo ya Yosefe yoimira Efuraimu+ komanso anzawo onse a nyumba ya Isiraeli.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena