Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 17:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Lankhula ndi ana a Isiraeli, ndipo utenge ndodo+ ya fuko lililonse kwa mtsogoleri+ wa fukolo. Zikhalepo ndodo 12. Pandodo iliyonse ulembepo dzina la mtsogoleri wa fukolo.

  • Ezekieli 37:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Uwauze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ine nditenga ndodo ya Yosefe imene ili m’dzanja la Efuraimu. Ndodo imeneyi ikuimiranso mafuko a Isiraeli omwe ndi anzake a Efuraimu. Ndidzaika mafukowo pandodo ya Yuda ndipo ndodo ziwirizo zidzakhala ndodo imodzi.+ Ndodozo zidzakhala ndodo imodzi m’dzanja langa.”’

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena