10 Asilikali othamangawo+ anapitiriza ulendo wawo ndipo anapita kumzinda ndi mzinda m’dziko lonse la Efuraimu+ ndi Manase mpaka ku Zebuloni. Koma anthuwo ankangokhalira kuwatonza ndi kuwaseka.+
6 Pakuti tsiku lidzafika, pamene alonda amene ali m’mapiri a Efuraimu adzafuula kuti, ‘Nyamukani amuna inu, tiyeni tipite ku Ziyoni, kwa Yehova Mulungu wathu.’”+