2 Mbiri 36:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma iwo ankangonyogodola+ amithenga a Mulungu woona, kunyoza mawu ake+ ndi kuseka+ aneneri ake, mpaka kufika poti panalibenso chiyembekezo choti angathe kuchiritsidwa.+ Kenako mkwiyo+ wa Yehova unawagwera. Machitidwe 17:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndiyeno anthuwo atamva za kuuka kwa akufa, ena anayamba kuseka monyodola,+ pamene ena anati: “Chabwino, udzatiuzenso zimenezi nthawi ina.”
16 Koma iwo ankangonyogodola+ amithenga a Mulungu woona, kunyoza mawu ake+ ndi kuseka+ aneneri ake, mpaka kufika poti panalibenso chiyembekezo choti angathe kuchiritsidwa.+ Kenako mkwiyo+ wa Yehova unawagwera.
32 Ndiyeno anthuwo atamva za kuuka kwa akufa, ena anayamba kuseka monyodola,+ pamene ena anati: “Chabwino, udzatiuzenso zimenezi nthawi ina.”