2 Mafumu 23:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Kuwonjezera apo, Farao Neko anaika Eliyakimu+ mwana wa Yosiya kukhala mfumu m’malo mwa Yosiya bambo ake, n’kumusintha dzina kuti akhale Yehoyakimu. Atatero anatenga Yehoahazi n’kupita naye ku Iguputo, kumene anakafa pamapeto pake.+ 2 Mbiri 36:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kuwonjezera apo, mfumu+ ya Iguputo inaika Eliyakimu+ m’bale wa Yehoahazi kukhala mfumu ya Yuda ndi Yerusalemu n’kumusintha dzina kuti akhale Yehoyakimu. Koma Yehoahazi m’bale wakeyo, Neko+ anam’tenga n’kupita naye ku Iguputo.+
34 Kuwonjezera apo, Farao Neko anaika Eliyakimu+ mwana wa Yosiya kukhala mfumu m’malo mwa Yosiya bambo ake, n’kumusintha dzina kuti akhale Yehoyakimu. Atatero anatenga Yehoahazi n’kupita naye ku Iguputo, kumene anakafa pamapeto pake.+
4 Kuwonjezera apo, mfumu+ ya Iguputo inaika Eliyakimu+ m’bale wa Yehoahazi kukhala mfumu ya Yuda ndi Yerusalemu n’kumusintha dzina kuti akhale Yehoyakimu. Koma Yehoahazi m’bale wakeyo, Neko+ anam’tenga n’kupita naye ku Iguputo.+