Yeremiya 30:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mkwiyo woyaka moto wa Yehova sudzatha kufikira atachita zofuna za mtima wake ndi kuzikwaniritsa.+ M’masiku otsiriza, anthu inu mudzalingalira zimenezi.+
24 Mkwiyo woyaka moto wa Yehova sudzatha kufikira atachita zofuna za mtima wake ndi kuzikwaniritsa.+ M’masiku otsiriza, anthu inu mudzalingalira zimenezi.+