Hoseya 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Yehova ali ndi mlandu woti aimbe Yuda.+ Adzalanga Yakobo mogwirizana ndi njira zake+ ndipo adzamubwezera mogwirizana ndi zochita zake.+
2 “Yehova ali ndi mlandu woti aimbe Yuda.+ Adzalanga Yakobo mogwirizana ndi njira zake+ ndipo adzamubwezera mogwirizana ndi zochita zake.+