Ekisodo 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwe uzimuuza zonse zimene ndizikulamula,+ koma Aroni m’bale wako azikulankhulira kwa Farao,+ ndipo adzaloladi ana a Isiraeli kuchoka m’dziko lake.+ Numeri 22:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Usikuwo Mulungu anafika kwa Balamu, n’kumuuza kuti: “Ngati anthuwa abwera kudzakuitana, nyamuka, pita nawo limodzi. Koma ukalankhule mawu okhawo amene ndikakuuze.”+ 2 Mbiri 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma Mikaya anati: “Pali Yehova Mulungu wamoyo,+ zimene Mulungu wanga anene n’zimene ndikalankhule.”+ Yeremiya 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Imvani mawu a pangano langa, anthu inu! “Anthu a ku Yuda komanso okhala mu Yerusalemu ukawauze+ mawu amenewa. Ezekieli 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye anapitiriza kundiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, pita pakati pa nyumba+ ya Isiraeli ndipo ukawauze mawu anga.
2 Iwe uzimuuza zonse zimene ndizikulamula,+ koma Aroni m’bale wako azikulankhulira kwa Farao,+ ndipo adzaloladi ana a Isiraeli kuchoka m’dziko lake.+
20 Usikuwo Mulungu anafika kwa Balamu, n’kumuuza kuti: “Ngati anthuwa abwera kudzakuitana, nyamuka, pita nawo limodzi. Koma ukalankhule mawu okhawo amene ndikakuuze.”+
13 Koma Mikaya anati: “Pali Yehova Mulungu wamoyo,+ zimene Mulungu wanga anene n’zimene ndikalankhule.”+
2 “Imvani mawu a pangano langa, anthu inu! “Anthu a ku Yuda komanso okhala mu Yerusalemu ukawauze+ mawu amenewa.
4 Iye anapitiriza kundiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, pita pakati pa nyumba+ ya Isiraeli ndipo ukawauze mawu anga.