Salimo 37:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Woipa amalondalonda munthu wolungama,+Ndipo amafuna kuti amuphe.+ Amosi 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘Anthuwo amadana ndi munthu wowadzudzula pachipata cha mzinda,+ komanso amanyansidwa ndi munthu wowauza chilungamo.+
10 “‘Anthuwo amadana ndi munthu wowadzudzula pachipata cha mzinda,+ komanso amanyansidwa ndi munthu wowauza chilungamo.+