Ezekieli 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Iwe mwana wa munthu, tenga njerwa ndipo uiike pamaso pako. Panjerwapo ujambulepo mzinda wa Yerusalemu.+ Ezekieli 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nena mwambi wokhudza nyumba yopanduka.+ Unene kuti:“‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ika pamoto mphika wakukamwa kwakukulu ndipo uthiremo madzi.+
4 “Iwe mwana wa munthu, tenga njerwa ndipo uiike pamaso pako. Panjerwapo ujambulepo mzinda wa Yerusalemu.+
3 Nena mwambi wokhudza nyumba yopanduka.+ Unene kuti:“‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ika pamoto mphika wakukamwa kwakukulu ndipo uthiremo madzi.+