Ezekieli 16:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 “‘Mkulu wako amene akukhala kumanzere kwako ndiye Samariya+ ndi midzi yake yozungulira.+ Mng’ono wako, amene akukhala mbali ya kudzanja lako lamanja ndi Sodomu+ ndi midzi yake yozungulira.+ Ezekieli 23:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Iwe mwana wa munthu, panali akazi awiri, ana aakazi obadwa kwa mayi mmodzi.+
46 “‘Mkulu wako amene akukhala kumanzere kwako ndiye Samariya+ ndi midzi yake yozungulira.+ Mng’ono wako, amene akukhala mbali ya kudzanja lako lamanja ndi Sodomu+ ndi midzi yake yozungulira.+