Yeremiya 51:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Wofunkha adzafikira Babulo+ ndipo amuna ake amphamvu adzagwidwa.+ Mauta awo adzathyoledwa,+ pakuti Yehova ndi Mulungu wobwezera.+ Iye adzawabwezera ndithu.+ Mika 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Dzanja lanu lidzakhala pamwamba pa adani anu,+ ndipo adani anu onse adzaphedwa.”+
56 Wofunkha adzafikira Babulo+ ndipo amuna ake amphamvu adzagwidwa.+ Mauta awo adzathyoledwa,+ pakuti Yehova ndi Mulungu wobwezera.+ Iye adzawabwezera ndithu.+