Mika 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Koma iwe nsanja ya gulu la nkhosa, malo okwera a mwana wamkazi wa Ziyoni,+ ulamuliro udzabwerera kwa iwe. Ulamuliro woyamba, ufumu wa mwana wamkazi wa Yerusalemu,+ udzabwerera kwa iwe.+
8 “Koma iwe nsanja ya gulu la nkhosa, malo okwera a mwana wamkazi wa Ziyoni,+ ulamuliro udzabwerera kwa iwe. Ulamuliro woyamba, ufumu wa mwana wamkazi wa Yerusalemu,+ udzabwerera kwa iwe.+