2 Samueli 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ngakhale zinali choncho, Davide analanda Ziyoni, malo okhala mumpanda wolimba kwambiri,+ umene ndi Mzinda wa Davide.+ Yesaya 10:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kukadali masana, iye aima ku Nobu.+ Ndi dzanja lake, iye akuopseza phiri la mwana wamkazi wa Ziyoni, phiri limene pali Yerusalemu.+
7 Ngakhale zinali choncho, Davide analanda Ziyoni, malo okhala mumpanda wolimba kwambiri,+ umene ndi Mzinda wa Davide.+
32 Kukadali masana, iye aima ku Nobu.+ Ndi dzanja lake, iye akuopseza phiri la mwana wamkazi wa Ziyoni, phiri limene pali Yerusalemu.+