Yeremiya 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndichiritseni inu Yehova, ndipo ndidzachiradi.+ Ndipulumutseni ndipo ndidzapulumukadi,+ pakuti ine ndimatamanda inu.+ Maliro 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Inu Yehova, tibwezeni+ kwa inu ndipo ife tibwerera mwamsanga. Mubwezeretse zinthu zonse kuti zikhale ngati mmene zinalili kale.+
14 Ndichiritseni inu Yehova, ndipo ndidzachiradi.+ Ndipulumutseni ndipo ndidzapulumukadi,+ pakuti ine ndimatamanda inu.+
21 Inu Yehova, tibwezeni+ kwa inu ndipo ife tibwerera mwamsanga. Mubwezeretse zinthu zonse kuti zikhale ngati mmene zinalili kale.+