Levitiko 27:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma ngati wapereka mundawo Chaka cha Ufulu chitadutsa, wansembe azimuwerengera mtengo wake mogwirizana ndi zaka zimene zatsala kukafika m’Chaka cha Ufulu chotsatira, ndipo azichotsera pa mtengo wake woikidwiratu.+
18 Koma ngati wapereka mundawo Chaka cha Ufulu chitadutsa, wansembe azimuwerengera mtengo wake mogwirizana ndi zaka zimene zatsala kukafika m’Chaka cha Ufulu chotsatira, ndipo azichotsera pa mtengo wake woikidwiratu.+