Levitiko 25:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ukamagula malo kwa mnzako, uziwerenga zaka zimene zapitapo kuchokera m’Chaka cha Ufulu. Azikugulitsa malowo mogwirizana ndi zaka zimene udzakhala ukukololapo.+ Levitiko 25:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ngati zaka zimene udzakhala ukukololapo n’zambiri, azikugulitsa pa mtengo wokwera,+ koma ngati zakazo zili zochepa azitsitsa mtengo wa malowo, chifukwa akukugulitsa mbewu zimene udzakhala ukukololapo. Levitiko 25:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 aziwerenga zaka zimene zapitapo kuchokera pamene anagulitsa malowo, ndipo azibweza ndalama zotsala kwa munthu amene anagula malowo. Akatero azibwerera kumalo akewo.+
15 Ukamagula malo kwa mnzako, uziwerenga zaka zimene zapitapo kuchokera m’Chaka cha Ufulu. Azikugulitsa malowo mogwirizana ndi zaka zimene udzakhala ukukololapo.+
16 Ngati zaka zimene udzakhala ukukololapo n’zambiri, azikugulitsa pa mtengo wokwera,+ koma ngati zakazo zili zochepa azitsitsa mtengo wa malowo, chifukwa akukugulitsa mbewu zimene udzakhala ukukololapo.
27 aziwerenga zaka zimene zapitapo kuchokera pamene anagulitsa malowo, ndipo azibweza ndalama zotsala kwa munthu amene anagula malowo. Akatero azibwerera kumalo akewo.+