Levitiko 25:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Iye aziwerengera wom’gulayo zaka zotsala kuchokera pamene anadzigulitsa kukafika Chaka cha Ufulu,+ ndipo ndalama zimene anam’gulira zizigwirizana ndi kuchuluka kwa zaka.+ Azim’gwirira ntchito mofanana ndi waganyu.+
50 Iye aziwerengera wom’gulayo zaka zotsala kuchokera pamene anadzigulitsa kukafika Chaka cha Ufulu,+ ndipo ndalama zimene anam’gulira zizigwirizana ndi kuchuluka kwa zaka.+ Azim’gwirira ntchito mofanana ndi waganyu.+