Levitiko 27:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ng’ombe kapena nkhosa iliyonse ya 10, pa nyama zonse zodutsa pansi pa ndodo,*+ iliyonse ya 10 iziperekedwa kwa Yehova ndipo izikhala yopatulika.
32 Ng’ombe kapena nkhosa iliyonse ya 10, pa nyama zonse zodutsa pansi pa ndodo,*+ iliyonse ya 10 iziperekedwa kwa Yehova ndipo izikhala yopatulika.