2 Mbiri 21:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Patatha zaka ziwiri zathunthu iye akudwala, matumbo ake+ anatuluka ndipo anamwalira ndi matenda oipawa. Anthu ake sanamupserezere zofukiza pa maliro ake ngati mmene anachitira+ pa maliro a makolo ake.
19 Patatha zaka ziwiri zathunthu iye akudwala, matumbo ake+ anatuluka ndipo anamwalira ndi matenda oipawa. Anthu ake sanamupserezere zofukiza pa maliro ake ngati mmene anachitira+ pa maliro a makolo ake.