Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 14:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pambuyo pake, munthu wina amene anathawa anafika kwa Abulamu Mheberi.+ Pa nthawiyo n’kuti Abulamu akukhala m’hema wake pakati pa mitengo ikuluikulu. Mitengoyo mwiniwake anali Mamure, yemwe anali Muamori.+ Ameneyu anali m’bale wake wa Esikolo, ndipo analinso m’bale wake wa Aneri.+ Iwowa anapanga ubale ndi Abulamu.

  • 2 Akorinto 11:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Kodi iwo ndi Aheberi? Inenso ndine Mheberi.+ Kodi ndi Aisiraeli? Inenso ndine Mwisiraeli. Kapena iwo ndi mbewu ya Abulahamu? Inenso chimodzimodzi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena