Genesis 14:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ineyo sinditengapo chilichonse ayi,+ koma zokhazo zimene anyamata anadya, komanso zogawira anyamata amene anapita nane. Amenewo ndi Aneri, Esikolo ndi Mamure.+ Aliyense atenge gawo lake.”+ Numeri 32:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwo atafika kuchigwa* cha Esikolo+ n’kuliona dzikolo, anatayitsa mtima ana a Isiraeli, kuti asakalowe m’dziko limene Yehova anatsimikiza mtima kuwapatsa.+
24 Ineyo sinditengapo chilichonse ayi,+ koma zokhazo zimene anyamata anadya, komanso zogawira anyamata amene anapita nane. Amenewo ndi Aneri, Esikolo ndi Mamure.+ Aliyense atenge gawo lake.”+
9 Iwo atafika kuchigwa* cha Esikolo+ n’kuliona dzikolo, anatayitsa mtima ana a Isiraeli, kuti asakalowe m’dziko limene Yehova anatsimikiza mtima kuwapatsa.+