2 Mbiri 36:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako Nebukadinezara+ mfumu ya Babulo anabwera+ kudzam’manga ndi zomangira ziwiri zamkuwa n’kupita naye ku Babulo.+ Danieli 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 M’chaka chachitatu cha ufumu wa Yehoyakimu+ mfumu ya Yuda, Nebukadinezara mfumu ya Babulo anabwera ku Yerusalemu ndipo anazungulira mzindawo.+
6 Kenako Nebukadinezara+ mfumu ya Babulo anabwera+ kudzam’manga ndi zomangira ziwiri zamkuwa n’kupita naye ku Babulo.+
1 M’chaka chachitatu cha ufumu wa Yehoyakimu+ mfumu ya Yuda, Nebukadinezara mfumu ya Babulo anabwera ku Yerusalemu ndipo anazungulira mzindawo.+