Deuteronomo 31:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma ine ndidzawabisira nkhope yanga pa tsiku limenelo chifukwa cha zoipa zonse zimene achita, chifukwa chotembenukira kwa milungu ina.+ Yeremiya 44:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma inu simunamvere+ kapena kutchera khutu lanu kuti musiye kuchita zinthu zoipa zomwe ndi kupereka nsembe zautsi kwa milungu ina.+
18 Koma ine ndidzawabisira nkhope yanga pa tsiku limenelo chifukwa cha zoipa zonse zimene achita, chifukwa chotembenukira kwa milungu ina.+
5 Koma inu simunamvere+ kapena kutchera khutu lanu kuti musiye kuchita zinthu zoipa zomwe ndi kupereka nsembe zautsi kwa milungu ina.+