2 Mbiri 36:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma iwo ankangonyogodola+ amithenga a Mulungu woona, kunyoza mawu ake+ ndi kuseka+ aneneri ake, mpaka kufika poti panalibenso chiyembekezo choti angathe kuchiritsidwa.+ Kenako mkwiyo+ wa Yehova unawagwera. Salimo 81:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma anthu anga sanamvere mawu anga.+Ndipo Isiraeli sanasonyeze kuti ndi wofunitsitsa kundimvera.+
16 Koma iwo ankangonyogodola+ amithenga a Mulungu woona, kunyoza mawu ake+ ndi kuseka+ aneneri ake, mpaka kufika poti panalibenso chiyembekezo choti angathe kuchiritsidwa.+ Kenako mkwiyo+ wa Yehova unawagwera.
11 Koma anthu anga sanamvere mawu anga.+Ndipo Isiraeli sanasonyeze kuti ndi wofunitsitsa kundimvera.+