Ekisodo 32:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mose ali m’phirimo, anthu anaona kuti akuchedwa kutsika.+ Chotero anthuwo anasonkhana kwa Aroni ndi kumuuza kuti: “Tipangire mulungu woti atitsogolere,+ chifukwa sitikudziwa zimene zachitikira Mose, amene anatitulutsa m’dziko la Iguputo.”+ Deuteronomo 32:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yesuruni*+ atayamba kunenepa, anayamba kupanduka.+Iwe wanenepa, wakulupala, wakhuta mopitirira muyezo.+Pamenepo iye anasiya Mulungu amene anam’panga,+Ndi kunyoza Thanthwe+ la chipulumutso chake.
32 Mose ali m’phirimo, anthu anaona kuti akuchedwa kutsika.+ Chotero anthuwo anasonkhana kwa Aroni ndi kumuuza kuti: “Tipangire mulungu woti atitsogolere,+ chifukwa sitikudziwa zimene zachitikira Mose, amene anatitulutsa m’dziko la Iguputo.”+
15 Yesuruni*+ atayamba kunenepa, anayamba kupanduka.+Iwe wanenepa, wakulupala, wakhuta mopitirira muyezo.+Pamenepo iye anasiya Mulungu amene anam’panga,+Ndi kunyoza Thanthwe+ la chipulumutso chake.