Deuteronomo 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Chotero musamale moyo wanu,+ chifukwa pa tsiku limene Yehova analankhula nanu kuchokera pakati pa moto ku Horebe, simunaone kalikonse+ m’motomo. Yohane 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mulungu ndiye Mzimu,+ ndipo onse omulambira ayenera kumulambira motsogoleredwa ndi mzimu ndi choonadi.”+ Machitidwe 7:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Anauza Aroni kuti, ‘Tipangire milungu ititsogolere. Chifukwa sitikudziwa zimene zachitikira Mose, amene anatitsogolera potuluka m’dziko la Iguputo.’+ Machitidwe 17:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Popeza kuti ndife mbadwa za Mulungu,+ tisaganize kuti Mulunguyo+ ali ngati golide, siliva, mwala kapena chilichonse chosemedwa mwa luso ndi nzeru za munthu.+
15 “Chotero musamale moyo wanu,+ chifukwa pa tsiku limene Yehova analankhula nanu kuchokera pakati pa moto ku Horebe, simunaone kalikonse+ m’motomo.
24 Mulungu ndiye Mzimu,+ ndipo onse omulambira ayenera kumulambira motsogoleredwa ndi mzimu ndi choonadi.”+
40 Anauza Aroni kuti, ‘Tipangire milungu ititsogolere. Chifukwa sitikudziwa zimene zachitikira Mose, amene anatitsogolera potuluka m’dziko la Iguputo.’+
29 “Popeza kuti ndife mbadwa za Mulungu,+ tisaganize kuti Mulunguyo+ ali ngati golide, siliva, mwala kapena chilichonse chosemedwa mwa luso ndi nzeru za munthu.+