Aefeso 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Kuti zinthu zikuyendere bwino, ndiponso kuti ukhale ndi moyo wautali padziko lapansi.”+ Akolose 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ananu, muzimvera+ makolo anu pa zinthu zonse, pakuti kuchita zimenezi kumakondweretsa Ambuye.