2 Mafumu 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehoyakini+ anali ndi zaka 18 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira miyezi itatu ku Yerusalemu.+ Mayi ake anali a ku Yerusalemu ndipo dzina lawo linali Nehusita mwana wa Elinatani. Yeremiya 26:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma Mfumu Yehoyakimu inatumiza Elinatani, mwana wa Akibori+ ndi amuna ena ku Iguputo.
8 Yehoyakini+ anali ndi zaka 18 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira miyezi itatu ku Yerusalemu.+ Mayi ake anali a ku Yerusalemu ndipo dzina lawo linali Nehusita mwana wa Elinatani.