Yeremiya 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Chonde tifunsire kwa Yehova+ chifukwa Nebukadirezara mfumu ya Babulo akufuna kumenyana nafe nkhondo.+ Mwina Yehova adzatichitira imodzi mwa ntchito zake zamphamvu kuti Nebukadirezarayo atichokere.”+
2 “Chonde tifunsire kwa Yehova+ chifukwa Nebukadirezara mfumu ya Babulo akufuna kumenyana nafe nkhondo.+ Mwina Yehova adzatichitira imodzi mwa ntchito zake zamphamvu kuti Nebukadirezarayo atichokere.”+