Yeremiya 26:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo ansembe ndi aneneri anayamba kuuza akalongawo ndi anthu onse kuti: “Munthu uyu akuyenera chiweruzo cha imfa+ chifukwa chakuti wanenera za mzinda uwu monga mmene mwamvera ndi makutu anu.”+
11 Pamenepo ansembe ndi aneneri anayamba kuuza akalongawo ndi anthu onse kuti: “Munthu uyu akuyenera chiweruzo cha imfa+ chifukwa chakuti wanenera za mzinda uwu monga mmene mwamvera ndi makutu anu.”+