Yeremiya 32:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa nthawi imeneyo, magulu ankhondo a mfumu ya Babulo anali atazungulira Yerusalemu.+ Ndipo mneneri Yeremiya anali atamutsekera m’nyumba imene inali m’Bwalo la Alonda.+ Bwalo limeneli linali pafupi ndi nyumba ya mfumu ya Yuda. Yeremiya 33:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Yeremiya atamutsekera m’Bwalo la Alonda,+ Yehova analankhula naye kachiwiri kuti:
2 Pa nthawi imeneyo, magulu ankhondo a mfumu ya Babulo anali atazungulira Yerusalemu.+ Ndipo mneneri Yeremiya anali atamutsekera m’nyumba imene inali m’Bwalo la Alonda.+ Bwalo limeneli linali pafupi ndi nyumba ya mfumu ya Yuda.