Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nehemiya 3:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndiyeno Palali mwana wamwamuna wa Uzai, anakonza mpandawo kutsogolo kwa Mchirikizo wa Khoma ndipo anakonzanso nsanja yochokera pa Nyumba ya Mfumu+ imene ili kumtunda m’Bwalo la Alonda.+ Kenako, Pedaya mwana wamwamuna wa Parosi,+ anakonza mpandawo kuchokera pamene Palali analekezera.

  • Yeremiya 33:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Yeremiya atamutsekera m’Bwalo la Alonda,+ Yehova analankhula naye kachiwiri kuti:

  • Yeremiya 37:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Chotero Mfumu Zedekiya inalamula kuti atsekere Yeremiya m’Bwalo la Alonda+ ndipo anali kumupatsa mtanda wobulungira wa mkate tsiku ndi tsiku. Mkate umenewu unali kuchokera kumsewu wa ophika mkate+ ndipo anapitiriza kum’patsa mkatewo kufikira mkate wonse utatha mumzindamo.+ Choncho Yeremiya anapitiriza kukhala m’Bwalo la Alonda.+

  • Yeremiya 38:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Yeremiya anapitirizabe kukhala m’Bwalo la Alonda+ kufikira tsiku limene Yerusalemu analandidwa.+ Mawu a Yeremiya anakwaniritsidwadi pamene Yerusalemu analandidwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena