Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 28:53
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 53 Pamenepo udzadya chipatso cha mimba yako, mnofu wa ana ako aamuna ndi ana ako aakazi,+ amene Yehova Mulungu wako wakupatsa, chifukwa cha zovuta ndi nsautso zimene adani ako adzakupanikiza nazo.

  • 2 Mafumu 25:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 M’mwezi wachinayi, pa tsiku la 9,+ njala+ inafika poipa kwambiri mumzindawo, ndipo anthu a m’dzikolo analibiretu chakudya.+

  • Yeremiya 38:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Inu mbuyanga mfumu, zimene anthu awa achitira mneneri Yeremiya ndi zoipa, chifukwa amuponya m’chitsime, ndipo afera momwemo+ chifukwa cha njala,+ pakuti mkate watheratu mumzindawu.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena