1 Mafumu 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Akhwangwala ankamubweretsera mkate ndi nyama m’mawa ndi madzulo, ndipo iye ankamwa madzi mumtsinje umene unali m’chigwacho.+ Salimo 37:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pa nthawi yatsoka sadzachita manyazi,+Ndipo pa nthawi ya njala adzakhuta.+
6 Akhwangwala ankamubweretsera mkate ndi nyama m’mawa ndi madzulo, ndipo iye ankamwa madzi mumtsinje umene unali m’chigwacho.+