2 Samueli 23:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Zalimoni Mwahohi,+ Maharai+ Mnetofa, 1 Mbiri 2:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Ana a Salima anali anthu okhala ku Betelehemu,+ ku Netofa,+ ndi ku Atiroti-beti-yowabu. Hafu ya anthu okhala ku Manahati ndi anthu okhala ku Zora, analinso ana a Salima. 1 Mbiri 11:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Maharai+ Mnetofa,+ Heledi+ mwana wa Bana Mnetofa,
54 Ana a Salima anali anthu okhala ku Betelehemu,+ ku Netofa,+ ndi ku Atiroti-beti-yowabu. Hafu ya anthu okhala ku Manahati ndi anthu okhala ku Zora, analinso ana a Salima.