Deuteronomo 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Uzichita chikondwerero cha misasa+ masiku 7, potuta zokolola kuchokera pamalo opunthira mbewu, pamalo oyengera mafuta ndi pamalo opondera mphesa. Yeremiya 39:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno ena mwa anthuwo, anthu onyozeka amene analibe kalikonse, Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu anawasiya m’dziko la Yuda,+ ndipo pa tsiku limenelo anawapatsa minda ya mpesa ndi ntchito zokakamiza kuti azigwira.+
13 “Uzichita chikondwerero cha misasa+ masiku 7, potuta zokolola kuchokera pamalo opunthira mbewu, pamalo oyengera mafuta ndi pamalo opondera mphesa.
10 Ndiyeno ena mwa anthuwo, anthu onyozeka amene analibe kalikonse, Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu anawasiya m’dziko la Yuda,+ ndipo pa tsiku limenelo anawapatsa minda ya mpesa ndi ntchito zokakamiza kuti azigwira.+