Yeremiya 40:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Nayenso Yohanani+ mwana wa Kareya+ ndi akuluakulu onse a magulu ankhondo amene anali m’madera a kunja kwa mzinda,+ anabwera kwa Gedaliya ku Mizipa.
13 Nayenso Yohanani+ mwana wa Kareya+ ndi akuluakulu onse a magulu ankhondo amene anali m’madera a kunja kwa mzinda,+ anabwera kwa Gedaliya ku Mizipa.