Yeremiya 41:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Patapita nthawi, Yohanani+ mwana wa Kareya ndi akuluakulu onse a magulu ankhondo+ amene anali naye anamva zoipa zonse zimene Isimaeli mwana wa Netaniya anachita. Yeremiya 42:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Kenako akuluakulu onse a magulu ankhondo, Yohanani+ mwana wa Kareya, Yezaniya+ mwana wa Hoshaya+ ndi anthu onse osasiyapo aliyense, anapita Yeremiya 43:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Azariya mwana wa Hoshaya,+ Yohanani+ mwana wa Kareya ndi anthu enanso odzikuza+ anauza Yeremiya kuti: “Ukunena zabodza. Yehova Mulungu wathu sanakutume kudzatiuza+ kuti, ‘Musapite ku Iguputo kuti mukakhale kumeneko monga alendo.’+
11 Patapita nthawi, Yohanani+ mwana wa Kareya ndi akuluakulu onse a magulu ankhondo+ amene anali naye anamva zoipa zonse zimene Isimaeli mwana wa Netaniya anachita.
42 Kenako akuluakulu onse a magulu ankhondo, Yohanani+ mwana wa Kareya, Yezaniya+ mwana wa Hoshaya+ ndi anthu onse osasiyapo aliyense, anapita
2 Azariya mwana wa Hoshaya,+ Yohanani+ mwana wa Kareya ndi anthu enanso odzikuza+ anauza Yeremiya kuti: “Ukunena zabodza. Yehova Mulungu wathu sanakutume kudzatiuza+ kuti, ‘Musapite ku Iguputo kuti mukakhale kumeneko monga alendo.’+