Yeremiya 40:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho akuluakulu amenewa anapita kwa Gedaliya ku Mizipa. Mayina awo anali Isimaeli+ mwana wa Netaniya, Yohanani+ ndi Yonatani ana a Kareya, Seraya mwana wa Tanumeti, ana a Efai Mnetofa,+ Yezaniya+ mwana wa Amaakati+ pamodzi ndi asilikali awo.+ Yeremiya 40:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Nayenso Yohanani+ mwana wa Kareya+ ndi akuluakulu onse a magulu ankhondo amene anali m’madera a kunja kwa mzinda,+ anabwera kwa Gedaliya ku Mizipa. Yeremiya 41:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Patapita nthawi, Yohanani+ mwana wa Kareya ndi akuluakulu onse a magulu ankhondo+ amene anali naye anamva zoipa zonse zimene Isimaeli mwana wa Netaniya anachita.
8 Choncho akuluakulu amenewa anapita kwa Gedaliya ku Mizipa. Mayina awo anali Isimaeli+ mwana wa Netaniya, Yohanani+ ndi Yonatani ana a Kareya, Seraya mwana wa Tanumeti, ana a Efai Mnetofa,+ Yezaniya+ mwana wa Amaakati+ pamodzi ndi asilikali awo.+
13 Nayenso Yohanani+ mwana wa Kareya+ ndi akuluakulu onse a magulu ankhondo amene anali m’madera a kunja kwa mzinda,+ anabwera kwa Gedaliya ku Mizipa.
11 Patapita nthawi, Yohanani+ mwana wa Kareya ndi akuluakulu onse a magulu ankhondo+ amene anali naye anamva zoipa zonse zimene Isimaeli mwana wa Netaniya anachita.