Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 41:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Patapita nthawi, Yohanani+ mwana wa Kareya ndi akuluakulu onse a magulu ankhondo+ amene anali naye anamva zoipa zonse zimene Isimaeli mwana wa Netaniya anachita.

  • Yeremiya 41:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndiyeno Yohanani+ mwana wa Kareya ndi akuluakulu onse a magulu ankhondo amene anali naye anatenga anthu onse otsala a ku Mizipa. Anthu amenewa anawalanditsa m’manja mwa Isimaeli mwana wa Netaniya amene anawagwira atapha Gedaliya+ mwana wa Ahikamu. Analanditsa amuna amphamvu, amuna ankhondo, akazi awo, ana ndi nduna za panyumba ya mfumu. Yohanani analanditsa anthu amenewa ku Gibeoni.

  • Yeremiya 42:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Kenako akuluakulu onse a magulu ankhondo, Yohanani+ mwana wa Kareya, Yezaniya+ mwana wa Hoshaya+ ndi anthu onse osasiyapo aliyense, anapita

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena