-
2 Mafumu 25:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Akuluakulu onse a magulu ankhondo+ ndi asilikali awo atamva kuti mfumu ya Babulo yasankha Gedaliya, nthawi yomweyo anapita kwa Gedaliya ku Mizipa.+ Akuluakuluwo anali Isimaeli mwana wa Netaniya, Yohanani mwana wa Kareya, Seraya mwana wa Tanumeti Mnetofa, ndi Yaazaniya mwana wa Amaakati, pamodzi ndi asilikali awo.
-