Yeremiya 40:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho akuluakulu amenewa anapita kwa Gedaliya ku Mizipa. Mayina awo anali Isimaeli+ mwana wa Netaniya, Yohanani+ ndi Yonatani ana a Kareya, Seraya mwana wa Tanumeti, ana a Efai Mnetofa,+ Yezaniya+ mwana wa Amaakati+ pamodzi ndi asilikali awo.+
8 Choncho akuluakulu amenewa anapita kwa Gedaliya ku Mizipa. Mayina awo anali Isimaeli+ mwana wa Netaniya, Yohanani+ ndi Yonatani ana a Kareya, Seraya mwana wa Tanumeti, ana a Efai Mnetofa,+ Yezaniya+ mwana wa Amaakati+ pamodzi ndi asilikali awo.+