Miyambo 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Munthu amene amadzikuza akapsa mtima, amatchedwa wodzikuza, wonyada ndi wodzitama.+ Miyambo 29:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kodi waona munthu wopupuluma m’mawu ake?+ Munthu wopusa ali ndi chiyembekezo chachikulu kuposa iyeyo.+
20 Kodi waona munthu wopupuluma m’mawu ake?+ Munthu wopusa ali ndi chiyembekezo chachikulu kuposa iyeyo.+