Salimo 123:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Moyo wathu wasautsika kwambiri chifukwa cha kunyoza kwa anthu amene akukhala mosatekeseka,+Ndiponso chifukwa cha kunyoza kwa anthu odzikuza.+ Miyambo 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kodi kudzikweza kwafika? Ndiye kuti manyazinso afika.+ Koma nzeru zimakhala ndi anthu odzichepetsa.+
4 Moyo wathu wasautsika kwambiri chifukwa cha kunyoza kwa anthu amene akukhala mosatekeseka,+Ndiponso chifukwa cha kunyoza kwa anthu odzikuza.+
2 Kodi kudzikweza kwafika? Ndiye kuti manyazinso afika.+ Koma nzeru zimakhala ndi anthu odzichepetsa.+