Yeremiya 42:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 mverani mawu a Yehova, inu otsala a Yuda. Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Ngati mwatsimikiza mtima kukakhala ku Iguputo ndipo mwalowadi m’dzikolo ndi kukhala kumeneko monga alendo,+
15 mverani mawu a Yehova, inu otsala a Yuda. Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Ngati mwatsimikiza mtima kukakhala ku Iguputo ndipo mwalowadi m’dzikolo ndi kukhala kumeneko monga alendo,+