-
Yeremiya 42:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 “Yehova Mulungu wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Monga mmene ndinasonyezera anthu okhala mu Yerusalemu+ mkwiyo ndi kupsa mtima kwanga, inunso ndidzakusonyezani mkwiyo wanga chifukwa chakuti mwakakhala ku Iguputo. Mudzakhala otembereredwa ndipo mudzakhala chinthu chodabwitsa ndi chotonzedwa,+ moti malo ano simudzawaonanso.’+
-