Yobu 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Amauza Mulungu woona kuti, ‘Chokani kwa ife!+Sitikufuna kudziwa njira zanu.+ Salimo 73:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Onani! Awa ndi anthu oipa, amene akukhala mosatekeseka mpaka kalekale.+Iwo achulukitsa chuma chawo.+
12 Onani! Awa ndi anthu oipa, amene akukhala mosatekeseka mpaka kalekale.+Iwo achulukitsa chuma chawo.+